
W/D ESTATE AGENCY
Malo ogulitsa ku Salima
Location : cornerstone
Kumpanda kuli manyumba 7
Kuli mjigo
Kuli tap
Kulinso chitsime
Magetsi ndi 100%
Kukula Kwa Malo 1 Acer
Komanso kunja Kwa mpanda kuli ma shop amene akugulitsira kumodzi
Mmbali mwa nsewu mweni mweni
Malo abwino a business
Mtengo ndi 39million
Call or wapp
0994458611
0888880056
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.









Leave a Reply