
BEARD GROWTH OIL
Oil wandenvuu uyuu
Original from komko
098 568 2208
Beard growth oil ndimafuta a tsitsi la abambo. Magutawa ndi opangidwa kuchokera ku zomera omwe amagwilisidwa Ntchito malo ngati;
Ndevu
Cheya chapa Chidali
Tsitsi la mmutu
Cheya chapa nkhungu
Tsitsi lakumalo obisika
Magutawa amagwira Ntchito;
Kumeletsa tsitsi kapena cheya pomwe palibe
Kukulisa tsitsi kapena Cheya
Kuteteza cheya kapena tsitsi kuma bacteria
Kusalalisa tsitsi kapena cheya
Kufewetsa tsitsi kapena cheya
Amatenga 2-4 days kuti uyambe kuwona zosatila zake
Akupezeka ku Blantyre ndipo kutali timatumiza
098 568 2208
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply