
Ameneyu ndi DYNANCE ROCENTA
ROCENTA ndi wachilengedwe ndipo amachiza matenda osachepera 400 , bola ngati nthendayo ili yosalodzedwa komanso ngati odwala atenga ROCENTA pa mlingo oyenelera molingana ndikukula kwa nthenda yake komanso kuti nthenda yakhalitsa motani.
DYNANCE ROCENTA ali ndi kuthekela kothana ndivuto lililonse chifukwa iye amalimbana ndi matenda pochotsa chomwe chikuyambitsa kudzela muma cells athupi lamunthu, amenewa ndima stem cells ochokela kuchilengedwe, omwe amakakonza ma cells athupi, pochotsa ma cells akufa, kumangaso chitetezo cha thupi, kulimbitsa ma cells omwe ngofowoka ndikuchulukitsa ma cells omwe ngabwino bwino kale.
ROCENTA akalowa m’thupi lamunthu amagawanika n’kupita pachiwalo chamuthupi chilichonse ndikuyamba kukonza mavuto…Read more
Contact +265 888 73 20 96
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.









Leave a Reply