
Salima
Mabwana Ndi Madona Pali ma shopu Ogulitsa Ku salima town Ali mbali mwasewu Pali ma shopu okwana 20 koma Ndi mashopu akulu akulu muli kale arent
Madzi magetsi zonse zilipo
Tilte deed ilipo zonse zoyeneleza zilipo
Pali space yayikulu
Zambiri tidzakambiran inu mukabwela
Akugulitsidwa pa mtengo okambirana WA
Mk195 million
Kuti mudziwe zambari imbana phone or WhatsApp Ku
+265888445394
+265994275337
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.










Leave a Reply