
Plot for sale at Lilongwe Chitedze.
Malowa ogulitsa kunoku Lilongwe Chitedze.
Malowa ndi 2 acres ndipo alikufupi Chitedze Day Secondary School.
Ngati mukufuna kugula maloku Lilongwe Chitedze alipo 2 acres madzi komaso magetsi zonse zilipo.
Akuyambira pa 16million kukambilana kulipo.
Mukafuna kuva zambiri ndiimbileni pa 0989849411.
Lilongwe Chitedze.
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply