
Gambusi izi almost new one,zatengeni changu kuno ku zomba sadzi,muzivala nthawi ya mvulayi komaso nthawi yokolora chimanga,size 7 komaso wa 8 atha kuvala,25 pin basi musawononge Nsapato nthawi ya mvula matope
Contact +265 998 48 95 30
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.
Leave a Reply