
+27 73 111 2112
*UTERINE FIBROIDS/ZOTUPA ZA MU CHIBEREKELO
Mthenda ina yomwe ikuzuza kwambiri amayi ndi imeneyi. Zotupa za mu chibelekelo.
Imaziwikaso kuti uterine leiomyomas (lie-omy-o-muhs, kutchula) “kapena myomas.
Mthenda iyi amayi ambiri akuvutika nayo kuchipatala apitaapitaso ikakula amangopanga operation.
Kuospya kwa operation kuli poti amathaso kusokoneza chibelekelo nde kuti ulendo obeleka wathela pompo
Vuto lomwe lilipo ambirinu ma herbs simuwasatila or simufuna kukhulupilira komano machilitso abwino ndi ma Herbal.
Uterine fibroids si cancer ndipo siimathela ku uterine cancer ndi zosiyana kotero osamaopa.
Zotupa zimenezi zimatha kukhala zambiri or chimozi. Nthawi chimakula mpaka mu rib cage kotero munthu umatha kunenepa kwa abdomal or kungofufuma mimba yokha.
…Read more
Add comment
You will be commenting as Guest.
Your email address will not be published.









Leave a Reply